Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 120:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji,Lilime lonyenga iwe?

4. Mibvi yakuthwa ya ciphona.Ndi makara tsanya.

5. Tsoka ine, kuti ndiri mlendo m'Meseke,Kuti ndigonera m'mahema a Kedara!

Werengani mutu wathunthu Masalmo 120