Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 120:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndinapfuulira kwa Yehova mu msauko wanga,Ndipo anandibvomereza,

2. Yehova, landitsani moyo wanga ku milomo ya mabodza,Ndi ku lilime lonyenga.

3. Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji,Lilime lonyenga iwe?

4. Mibvi yakuthwa ya ciphona.Ndi makara tsanya.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 120