Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 12:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Mau a Yehova ndi mau oona;Ngati siliva woyenga m'ng'anjo yadothi,Yoiyeretsa kasanu ndi kawiri.

7. Mudzawasunga, Yehova,Mudzawacinjirizira mbadwo uno ku nthawi zonse.

8. Oipa amayenda mozungulira-zungulira,Potamanda iwo conyansa mwa ana a anthu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 12