Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 119:61-63 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

61. Anandikulunga nazo zingwe za oipa;Koma sindinaiwala cilamulo canu.

62. Pakati pa usiku ndidzauka kukuyamikaniCifukwa ca maweruzo anu olungama.

63. Ine ndine wakuyanjana nao onse akukuopani,Ndi iwo akusamalira malangizo anu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 119