Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 119:38-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Limbitsirani mtumiki wanu mau anu,Ndiye wodzipereka kukuopani.

39. Mundipatutsire cotonza canga ndiciopaco;Popeza maweruzo anu ndi okoma.

40. Taonani, ndinalira malangizo anu;Mundipatse moyo mwa cilungamo canu.

41. Ndipo cifundo canu cindidzere, Yehova,Ndi cipulumutso canu, monga mwa mau anu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 119