Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 119:175-176 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

175. Mzimu wanga ukhale ndi moyo, ndipo udzakulemekezani;Ndipo maweruzo anu andithandize.

176. Ndinasocera ngati nkhosa yotayika; funani mtumiki wanu;Pakuti sindiiwala malamulo anu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 119