Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 119:13-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Ndinafotokozera ndi milomo yangaMaweruzo onse a pakamwa panu,

14. Ndinakondwera m'njira ya mboni zanu,Koposa ndi cuma conse,

15. Ndidzalingirira pa malangizo anu,Ndi kupenyerera mayendedwe anu.

16. Ndidzadzikondweretsa nao malemba anu;Sindidzaiwala mau anu,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 119