Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 117:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Lemekezani Yehova, amitundu onse;Myimbireni, anthu onse.

2. Pakuti cifundo cace ca pa ife ndi cacikuru;Ndi coonadi ca Yehova ncosatha.Haleluya.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 117