Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 116:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndidzapereka kwa Inu nsembe yaciyamiko,Ndipo ndidzaitanira dzina la Yehova.

18. Ndidzacita zowinda zanga za kwa Yehova,Tsopano, pamaso pa anthu ace onse;

19. M'mabwalo a nyumba ya Yehova,Pakati pa inu, Yerusalemu. Haleluya.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 116