Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 116:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndimkonda, popeza Yehova amamva,Mau anga ndi kupemba kwanga.

2. Popeza amandicherera khutu lace,Cifukwa cace ndidzaitanira Iye masiku anga onse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 116