Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 115:6-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Makutu ali nao, koma osamva;Mphuno ali nazo, koma osanunkhiza;

7. Manja ali nao, koma osagwira;Mapazi ali nao, koma osayenda;Kapena sanena pammero pao,

8. Adzafanana nao iwo akuwapanga;Ndi onse akuwakhulupirira,

9. Israyeli, khulupirira Yehova:Ndiye mthandizi wao ndi cikopa cao.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 115