Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 114:7-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Unjenjemere, dziko lapansi iwe, pamaso pa Ambuye,Pamaso pa Mulungu wa Yakobo;

8. Amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi,Nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 114