Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 114:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. M'mene Israyeli anaturuka ku Aigupto,Nyumba ya Yakobo kwa anthu a cinenedwe cacilendo;

2. Yuda anakhala malo ace oyera, Israyeli ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 114