Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 112:9-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Anagawagawa, anapatsa aumphawi;Cilungamo cace cikhalitsa kosatha;Nyanga yace idzakwezeka ndi ulemu.

10. Woipa adzaziona, nadzapsa mtima;Adzakukuta mano, nadzasungunuka;Cokhumba oipa cidzatayika.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 112