Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 111:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Haleluya.Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse,Mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano.

2. Nchito za Yehova nzazikuru,Zofunika ndi onse akukondwera nazo.

3. Cocita Iye nca ulemu, ndi ukuru:Ndi cilungamo cace cikhalitsa kosatha.

4. Anacita cokumbukitsa zodabwiza zace;Yehova ndiye wa cisomo ndi nsoni zokoma.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 111