Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 110:6-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Adzaweruza mwa amitundu,Adzadzaza dziko ndi mitembo;Adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.

7. Adzamwa ku mtsinje wa panjira;Cifukwa cace adzaweramutsa mutu wace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 110