Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 108:9-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Moabu ndiye mkhate wanga;Pa Edomu ndidzaponya nsapato yanga;Ndidzapfuulira Filistiya,

10. Adzandifikitsa ndani m'mudzi wa m'linga?Adzanditsogolera ndani ku Edomu?

11. Si ndinu Mulungu, amene mwatitayaOsaturuka nao magulu athu?

12. Tithandizeni mumsauko;Pakuti cipulumutso ca munthu ndi cabe.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 108