Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 108:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Wakhazikika mtima wanga, Mulungu;Ndidzayimba, inde ndidzayimba zolemekeza, ndiko ulemerero wanga.

2. Galamukani, cisakasa ndi zeze;Ndidzauka ndekha mamawa.

3. Ndidzakuyamikani mwa mitundu ya anthu, Yehova:Ndipo ndidzayimba zakukulemekezani mwa anthu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 108