Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 107:40-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

40. Atsanulira cimpepulo pa akulu,Nawasokeretsa m'cipululu mopanda njira.

41. Koma aika waumphawi pamsanje posazunzika,Nampatsa mabanja ngati gulu la nkhosa.

42. Oongoka mtima adzaciona nadzasekera;Koma cosalungama conse citseka pakamwa pace.

43. Wokhala nazo nzeru asamalire izi,Ndipo azindikire zacifundo za Yehova,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 107