Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 107:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Anasokera m'cipululu, m'njira yopanda anthu;Osapeza mudzi wokhalamo.

5. Anamva njala ndi ludzu,Moyo wao unakomoka m'kati mwao.

6. Pamenepo anapfuulira kwa Yehova mumsauko mwao,Ndipo anawalanditsa m'kupsinjika kwao.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 107