Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 107:18-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Mtima wao unyansidwa naco cakudya ciri conse;Ndipo ayandikira zipata za imfa.

19. Pamenepo apfuulira kwa Yehova m'kusauka kwao,Ndipo awapulumutsa m'kupsinjika kwao.

20. Atumiza mau ace nawaciritsa,Nawapulumutsa ku cionongeko cao.

21. Ayamike Yehova cifukwa ca cifundo cace,Ndi zodabwiza zace za kwa ana a anthu!

Werengani mutu wathunthu Masalmo 107