Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 106:30-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Pamenepo panauka Pinehasi, nacita cilango:Ndi mliriwo unaletseka.

31. Ndipo adamuyesa iye wacilungamo,Ku mibadwo mibadwo ku nthawi zonse.

32. Anautsanso mkwiyo wace ku madzi a Meriba,Ndipo kudaipira Mose cifukwa ca iwowa:

Werengani mutu wathunthu Masalmo 106