Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 106:25-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Koma anadandaula m'mahema mwao,Osamvera mau a Yehova.

26. Potero anawasamulira dzanja lace,Kuti awagwetse m'cipululu:

27. Kugwetsanso mbeu zao mwa amitundu,Ndi kuwabalalitsa m'maiko maiko.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 106