Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 106:11-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Ndipo madziwo anamiza owasautsa;Sanatsala mmodzi yense.

12. Pamenepo anabvomereza mau ace;Anayimbira comlemekeza.

13. Koma anaiwala nchito zace msanga;Sanalindira uphungu wace:

14. Popeza analaka-lakatu kucidikhako,Nayesa Mulungu m'cipululu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 106