Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 105:43-45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Potero anaturutsa anthu ace ndi kusekerera,Osankhika ace ndi kupfuula mokondwera.

44. Ndipo anawapatsa maiko a amitundu;Iwo ndipo analanda zipatso za nchito ya anthu:

45. Kuti asamalire malemba ace,Nasunge malamulo ace.Haleluya.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 105