Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 102:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, imvani pemphero langa,Ndipo mpfuu wanga ufikire Inu.

2. Musandibisire nkhope yanu tsiku la nsautso yanga;Mundichereze khutu lanu;Tsiku limene ndiitana ine mundiyankhe msanga,

3. Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi,Ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 102