Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 10:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Yehova, mwamva cikhumbo ca ozunzika:Mudzakhazikitsa mtima wao, mudzachereza khutu lanu:

18. Kuti muweruze mlandu wa amasiye ndi wokhalira mphanthi,Kuti munthu wa pa dziko lapansi angaonjeze kuopsa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 10