Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Muimiranji patari, Yehova?Mubisaliranji m'nyengo za nsautso?

2. Podzikuza woipa apsereza waumphawi;Agwe m'ciwembu anapanganaco.

3. Pakuti woipa adzitamira cifuniro ca moyo wace,Adalitsa wosirira, koma anyoza Yehova.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 10