Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 3:64-66 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

64. Mudzawabwezera cilango, Yehova, monga mwa macitidwe a manja ao;

65. Muphimbe mtima wao ndi kuwatemberera;

66. Mudzawalondola mokwiya ndi kuwaononga pansi pa thambo la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Maliro 3