Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 3:49-52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

49. Diso langa lingotsanulira osaleka, osapumula,

50. Kufikira Yehova adzazolika kumwamba ndi kuona;

51. Diso langa limvetsa moyo wanga zowawa cifukwa ca ana akazi onse a m'mudzi mwanga.

52. Ondida opanda cifukwa anandiinga ngati mbalame;

Werengani mutu wathunthu Maliro 3