Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tauka, tapfuula usiku, poyamba kulonda;Tsanulira mtima wako ngati madzi pamaso pa Ambuye;Takwezera maso ako kwa Iye, cifukwa ca moyo wa tiana tako,Timene tilefuka ndi njala pa malekezero a makwalala onse.

Werengani mutu wathunthu Maliro 2

Onani Maliro 2:19 nkhani