Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikucitire umboni wotani? ndikuyerekeze ndi ciani, mwana wamkazi wa Yerusalemu?Ndikulinganize ndi ciani kuti ndikutonthoze, namwaliwe, mwana wamkazi wa Ziyoni?Popeza akula ngati nyanja; ndani angakucize?

Werengani mutu wathunthu Maliro 2

Onani Maliro 2:13 nkhani