Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Maliro 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maso anga alefuka ndi misozi, m'kati mwanga mugwedezeka;Ciwindi canga cagwa pansi cifukwa ca kupasuka kwa mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga;Cifukwa tiana ndi oyamwa akomoka m'makwalala a mudziwu.

Werengani mutu wathunthu Maliro 2

Onani Maliro 2:11 nkhani