Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga mafuta onse a pamatumbo, ndi cokuta ca mphafa, ndi imso ziwiri, ndi mafuta ace, ndipo Mose anazitentha pa guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:16 nkhani