Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndatengako kwa ana a Israyeli, ku nsembe zoyamika zao, nganga ya nsembe yoweyula, ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja wa nsembe yokweza; ndipo ndazipereka kwa Aroni wansembe ndi kwa ana ace, zikhale zoyenera iwo kosatha zocokera kwa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:34 nkhani