Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu akakhudza cinthu codetsa, codetsa ca munthu, kapena codetsa ca zoweta, kapena ciri conse conyansa codetsa, nakadyako nyama ya nsembe zoyamika za Yehova, munthuyo asadzidwe kwa anthu a mtundu wace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:21 nkhani