Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akadyako nyama ya nsembe zoyamika zace tsiku lacitatu, sikubvomerezeka kumene; sadzamwerengera wobwera nayo; ndiyo cinthu conyansa, ndipo munthu wakudyako adzasenza mphulupulu zace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:18 nkhani