Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atengeko wodzala manja pa ufa wa copereka ca ufa wosalala, ndi pa mafuta ace, ndi libona lonse liri pa copereka caufa, nazitenthe pa guwa la nsembe, zicite pfungo lokoma, ndizo cikumbutso cace ca kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:15 nkhani