Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cuma cace cikapanda kufikira nkhosa, wocimwayo adze nayo kwa Yehova nsembe yace yoparamula, njiwa ziwiri, kapena maunda awiri; imodzi ikhale ya nsembe yaucimo, ndi yina ya nsembe yopsereza.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 5

Onani Levitiko 5:7 nkhani