Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembeyo atengeko mwazi, nauike pa nyanga za guwa la nsembe la cofukiza ca pfungo lokoma, lokhala m'cihema cokomanako pamaso pa Yehova; nathire mwazi wonse wa ng'ombeyo patsinde pa guwa la nsembe yopsereza, lokhala pa khomo la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:7 nkhani