Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naike mwazi wina pa nyanga za guwa la nsembe, lokhala pamaso pa Yehova, lokhala m'cihema cokomanako; nathire mwazi wonse patsinde pa guwa la nsembe yopsereza, lokhala pa khomo la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:18 nkhani