Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo khamu lonse la Israyeli likalakwa osati dala, ndipo cikabisika cinthuci pamaso pa msonkhano, litacita cina ca zinthu ziri zonse aziletsa Yehova, ndi kuparamula;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:13 nkhani