Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 27:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cuma cace cikapanda kufikira kuyesa kwako, amuike pamaso pa wansembe, kuti wansembeyo amuyese; ndipo wansembeyo amuyese, monga akhoza iye amene anawinda.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:8 nkhani