Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 27:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukayesa wamwamuna wa zaka makumi awiri kufikira wina wa zaka makumi asanu ndi limodzi, uziwayesera a masekeli makumi asanu a siliva, monga mwa sekeli wa malo opatulika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:3 nkhani