Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 27:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu woyamba kubadwa mwa nyama akhale wobadwa woyamba wa Yehova, munthu asampatule; ingakhale ng'ombe ingakhale nkhosa, ndiye wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:26 nkhani