Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 27:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akapatula nyumba yace ikhale yopatulika kwa Yehova, wansembe aziiyesa mtengo wace, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga wansembeyo aiyesa, ikhale momwemo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:14 nkhani