Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyengo yopuntha tirigu idzafikira nyengo yochera mphesa, ndi nyengo yochera mphesa idzafikira nyengo zobzala; ndipo mudzakhuta naco cakudya canu, ndi kukhala m'dziko mwanu okhazikika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:5 nkhani