Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo ndidzakumbukila pangano langa ndi Yakobo; ndiponso pangano langa ndi Isake, ndiponso pangano langa ndi Abrahamu ndidzakumbukila; ndipo ndidzakumbukila dzikoli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:42 nkhani