Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunena za iwo akutsalira, ndidzalonga kukomoka kumtima kwao m'maiko a adani ao; ndi liu la tsamba lotengeka ndi mphepo lidzawapitikitsa; ndipo adzathawa monga amathawa lupanga; ndipo adzagwa wopanda wakuwalondola.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:36 nkhani