Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza ndidzatumiza cirombo ca kuthengo pakati pa inu, ndipo cidzalanda ana anu, ndi kuononga zoweta zanu nicidzacepetsa inu kuti mukhale pang'ono; ndi njira zanu zidzakhala zakufa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:22 nkhani